John 16:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzakudulani ku mpingo. Komanso nthaŵi ilikudza yakuti aliyense amene adzakuphani, adzayesa kuti akutumikira Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzakutulutsani m'masunagoge, koma ikudza nthawi imene yense wakupha inu adzayesa kuti atumikira Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo adzakuchotsani mʼsunagoge mwawo. Kunena zoona, nthawi ikubwera imene aliyense amene adzakuphani adzaganiza kuti akutumikira Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzakuturutsani m'masunagoge; koma ikudza nthawi imene yense wakupha inu adzayesa kuti atumikira Mulungu,