John 16:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndakuuzani zimenezi mophiphiritsa. Nthaŵi ilikudza pamene sindidzalankhula nanunso mophiphiritsa, koma ndidzakudziŵitsani momveka za Atate.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zinthu izi ndalankhula ndi inu m'mafanizo; ikudza nthawi imene sindidzalankhula ndi inu m'mafanizo, koma ndidzakulalikirani inu m'mafanizo, koma ndidzakulalikirani inu momveka za Atate.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngakhale ndakhala ndikuyankhula mʼmafanizo, nthawi ikubwera imene Ine sindidzagwiritsanso ntchito mafanizo otere koma ndidzakuwuzani momveka za Atate anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zinthu izi ndalankhula ndi inu m'mafanizo; ikudza nthawi imene sindidzalankhula ndi inu m'mafanizo, koma ndidzakulalikirani inu momveka za Atate.