John 16:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzachita zimenezi chifukwa sadadziŵe Atate kapenanso Ine.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo izi adzachita, chifukwa sanadziwa Atate, kapena Ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo adzachita zoterozo chifukwa sanadziwe Atate kapena Inenso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo izi adzacita, cifukwa sanadziwa Atate, kapena Ine.