John 16:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma tsopano ndikupita kwa amene adandituma, ndipo palibe ndi mmodzi yemwe mwa inu wondifunsa kuti, ‘Mukupita kuti?’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma tsopano ndimuka kwa Iye wondituma Ine; ndipo palibe wina mwa inu andifunsa Ine, Munka kuti?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsopano Ine ndikupita kwa Iye amene anandituma koma palibe wina mwa inu akundifunsa kuti, ‘Kodi mukupita kuti?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma tsopano ndimuka kwa iye wondituma Ine; ndipo palibe wina mwa inu andifunsa Ine, Munka kuti?