John 17:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zanga zonse nzanu, monga zanu zonse nzanga, motero ndimalemekezedwa mwa iwowo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa ali anu: ndipo zanga zonse zili zanu, ndi zanu zili zanga; ndipo ndilemekezedwa mwa iwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zonse zimene Ine ndili nazo ndi zanu, ndipo zonse zimene Inu muli nazo ndi zanga. Choncho Ine ndalemekezedwa mwa iwowo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cifukwa ali anu: ndipo zanga zonse ziri zanu, ndi zanu ziri zanga; ndipo ndilemekezedwa mwa iwo.