John 17:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene ndinali nawo pamodzi, ndinkaŵasunga ndi mphamvu za dzina lanu, zimene mudandipatsa. Ndidaŵalondoloza bwino, ndipo palibe ndi mmodzi yemwe amene adatayika, kupatula yekha uja amene adayenera kutayika, kuti zipherezere zimene Malembo adaaneneratu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene ndinakhala nao, Ine ndinalikuwasunga iwo m'dzina lanu amene mwandipatsa Ine; ndipo ndinawasunga, ndipo sanatayika mmodzi yense wa iwo, koma mwana wa chitayiko, kuti lembo likwaniridwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene ndinali nawo, ndinawateteza ndi kuwasunga mosamala mʼdzina limene munandipatsa. Palibe ndi mmodzi yemwe amene anatayika kupatula yekhayo amene anayenera kuwonongeka kuti malemba akwaniritsidwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenendinakhala nao, Ine ndinalikuwasunga iwo m'dzina lanu amene mwandipatsa Ine; ndipo ndinawasunga, ndipo sanatayika mmodzi yense wa iwo, koma mwana wa citayiko, kuti lembo likwaniridwe.