John 17:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo sali a dziko lapansi, monga Inenso sindili wa dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Siali a dziko lapansi monga Ine sindili wa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo si a dziko lapansi, monga Ine sindilinso wa dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Siali adziko lapansi monga Ine sindiri wa dziko lapansi.