John 17:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga mudandituma Ine pansi pano, Inenso ndaŵatuma pansi pano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga momwe munandituma Ine kudziko lapansi, Inenso ndinatuma iwo kudziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga Inu munandituma Ine mʼdziko lapansi, Inenso ndikuwatuma mʼdziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga momwe munandituma Ine ku dziko lapansi, Inenso ndinatuma iwo ku dziko lapansi,