John 17:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Sindikupempherera iwo okhaŵa ai, komanso amene adzandikhulupirira chifukwa cha mau ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma sindipempherera iwo okha, komanso iwo akukhulupirira Ine chifukwa cha mau ao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ine sindikupempherera iwo okhawa, komanso amene adzandikhulupirira chifukwa cha uthenga wawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma sindipempherera iwo okha, komanso iwo akukhulupirira Ine cifukwa ca mau ao;