John 17:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atate olungama, anthu odalira zapansipano sadakudziŵeni ai, koma Ine ndimakudziŵani, ndipo aŵa ali panoŵa akudziŵa kuti ndinu mudandituma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atate wolungama, dziko lapansi silinadziwa Inu, koma Ine ndinadziwa Inu; ndipo iwo anazindikira kuti munandituma Ine;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Atate wolungama, ngakhale kuti dziko lapansi silikudziwani Inu, Ine ndimakudziwani, ndipo iwo amadziwa kuti Inu munandituma Ine.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atate wolungama, 3 dziko lapansi silinadziwa Inu, koma 4 Ine ndinadziwa Inu; ndipo 5 iwo anazindikira kuti munandituma Ine;