John 17:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndakulemekezani pansi pano pakutsiriza ntchito imene mudandipatsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ine ndalemekeza Inu pa dziko lapansi, m'mene ndinatsiriza ntchito imene munandipatsa ndichite.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndabweretsa ulemerero wanu pa dziko pamene ndamaliza ntchito imene munandipatsa kuti ndi igwire.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ine ndalemekeza Inu pa dziko lapansi, m'mene ndinatsiriza nchito imene munandipatsa ndicite.