John 18:39 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma potsata chizoloŵezi chanu, pa nthaŵi ya chikondwerero cha Paska ndimakumasulirani mkaidi mmodzi. Tsono kodi mukufuna kuti ndikumasulireni Mfumu ya Ayudayi?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma muli nao makhalidwe, akuti ndimamasulira inu mmodzi pa Paska; kodi mufuna tsono kuti ndimasulire inu mfumu ya Ayuda?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ndi mwambo wanu kuti pa nthawi ya Paska, ine ndikumasulireni wamʼndende mmodzi. Kodi mufuna ndikumasulireni ‘Mfumu ya Ayuda?’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma muli nao makhalidwe, akuti ndimamasulira inu mmodzi pa Paskha; kodi mufuna tsono kuti ndimasulire inu Mfumu ya Ayuda?