John 19:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumeneko adampachika pa mtanda. Adapachikanso anthu ena aŵiri, wina ku dzanja lake lamanja, wina ku dzanja lake lamanzere, Yesu pakati.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kumene anampachika Iye; ndipo pamodzi ndi Iye awiri ena, chakuno ndi chauko, koma Yesu pakati.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo iwo anamupachika Iye pamodzi ndi anthu ena awiri, mmodzi mbali ina ndi wina mbali inanso ndipo Yesu pakati.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kumene anampacika Iye; ndipo pamodzi ndi iye awiri ena, cakuno ndi cauko, koma Yesu pakati.