John 19:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
nadza kwa Iye nkumanena kuti, “Tikuwoneni, mfumu ya Ayuda!” Ndipo adayamba kumuwomba makofi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nadza kwa Iye, nanena, Tikuoneni, mfumu ya Ayuda! Nampanda khofu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo ankapita kwa Iye mobwerezabwereza ndi kumanena kuti, “Moni mfumu ya Ayuda?” Ndipo amamumenya makofi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nadza kwa iye, nanena, Tikuoneni, Mfumu ya Ayuda! nampanda khofu.