John 19:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo penanso Malembo akuti, “Anthu azidzamuyang'ana amene iwo adamubaya.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo linenanso lembo lina, Adzayang'ana pa Iye amene anampyoza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi monga lemba linanso linena, “Iwo adzayangʼana Iye amene iwo anamubaya.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo linenanso lembo lina, 5 Adzayang'ana pa iye amene anampyoza.