John 19:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Yesu adatuluka, atavala nsangamutu ija ndi chovala chofiirira chija, Pilato adati, “Nayutu munthu uja.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Yesu anatuluka kunja, atavala korona waminga, ndi malaya achibakuwa. Ndipo ananena nao, Taonani munthuyu!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo Yesu anatuluka atavala nkhata yaminga ndi mkanjo wapepo ndipo Pilato anawawuza kuti, “Nayu munthu uja!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Yesu anaturuka kunja, atabvala korona waminga; ndi maraya acibakuwa, Ndipo ananena nao, Taonani munthuyu!