John 2:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo amai ake adauza anyamata amene ankatumikira kuti, “Chilichonse chimene akuuzeni, muchite.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amake ananena kwa atumiki, Chimene chilichonse akanena kwa inu, chitani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amayi ake anati kwa antchito, “Inu muchite chilichonse chimene akuwuzeni.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amace ananena kwa atumiki, Cimene ciri conse akanena kwa inu, citani.