John 3:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wina wa m'gulu la Afarisi, dzina lake Nikodemo, mkulu wa Ayuda,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma panali munthu wa Afarisi, dzina lake Nikodemo, mkulu wa Ayuda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo panali Mfarisi wotchedwa Nekodimo, wa mʼgulu lolamulira la Ayuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma panali munthu wa Afarisi, dzina lace Nikodemo, mkulu wa Ayuda,