John 3:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Wochokera Kumwamba ali pamwamba pa onse. Wochokera pansi pano ndi wapansipano, ndipo amalankhula zapansipano. Wochokera Kumwamba ali pamwamba pa onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye wochokera Kumwamba ali woposa onse; iye amene ali wa dziko lapansi ali wa dziko lapansi, nalankhula za dziko lapansi: Iye wochokera Kumwamba ali woposa onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iye wochokera kumwamba ndi wapamwamba pa onse: iye wochokera mʼdziko lapansi ndi wa dziko lapansi, ndipo amayankhula monga mmodzi wa adziko lapansi. Iye wochokera kumwamba ndi wopambana onse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye wocokera Kumwamba ali woposa onse; iye amene ali wa dziko lapansi ali wa dziko lapansi, nalankhula za dziko lapansi: Iye wocokera Kumwamba ali woposa onse.