John 3:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iyeyu akuchitira umboni zimene adaziwona ndi kuzimva komabe palibe amene amakhulupirira mau akewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chimene anachiona nachimva, achita umboni wa ichi chomwe; ndipo kulibe munthu alandira umboni wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye achita umboni pa zimene waziona ndi kuzimva, koma palibe avomereza umboni wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cimene anaciona nacimva, acita umboni wa ici comwe; ndipo kulibe munthu alandira umboni wace.