John 3:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma munthu akakhulupirira mau akeŵo, pamenepo amatsimikiza kuti Mulungu sanama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye amene analandira umboni wake anaikapo chizindikiro chake kuti Mulungu ali woona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu amene amawulandira akutsimikizira kuti Mulungu ndi woona.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
1 Iye amene analandira umboni wace anaikapo cizindikilo cace kuti Mulungu ali woona.