John 3:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu Atate amakonda Mwana wake, ndipo adaika zonse m'manja mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atate akonda Mwana, nampatsa zinthu zonse m'dzanja lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atate amakonda Mwana ndipo apereka zonse mʼmanja mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
4 Atate akonda Mwana, nampatsa zinthu zonse m'dzanja lace.