John 3:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nikodemo adamufunsa kuti, “Kodi munthu angathe kubadwanso bwanji atakalamba kale? Kodi nkukaloŵa m'mimba mwa amai ake kuti abadwe kachiŵiri?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nikodemo ananena kwa Iye, Munthu akhoza bwanji kubadwa atakalamba? Kodi akhoza kulowanso m'mimba ya amake ndi kubadwa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nekodimo anati, “Kodi munthu angabadwenso bwanji atakalamba? Kodi angalowe kachiwiri mʼmimba ya amayi ake kuti abadwenso?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nikodemoananena kwa iye, Munthu akhoza bwanji kubadwa atakalamba? Kodi akhoza kulowanso m'mimba ya amace ndi kubadwa?