John 3:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nikodemo adafunsa kuti, “Zimenezi zingachitike bwanji?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nikodemo anayankha nati kwa Iye, Izi zingatheke bwanji?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nekodimo anafunsa kuti, “Kodi izi zingatheke bwanji?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nikodemo anayankha nati kwa iye, Izi zingatheke bwanji?