John 4:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maiyo adasiya mtsuko wake napita ku mudzi nkukauza anthu kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mkazi anasiya mtsuko wake, namuka kumudzi, nanena ndi anthu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka mayiyo anasiya mtsuko wamadzi, nabwerera ku mzinda ndipo anati kwa anthu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mkazi anasiya mtsuko wace, namuka kumudzi, nanena ndi anthu,