John 4:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi imeneyo ophunzira ake a Yesu ankamupempha kuti, “Aphunzitsi, idyani.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pa mphindikati iyi ophunzira ake anampempha Iye, ndi kunena, Rabi, idyani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nthawi imeneyi ndi kuti ophunzira ake akumukakamiza kuti, “Rabi idyani.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pa mphindikati iyi ophunzira ace anampempha iye, ndi kunena, Rabi, idyani.