John 4:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Iye adati, “Ine ndili nacho chakudya chimene inu simukuchidziŵa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Iye anati kwa iwo, Ine ndili nacho chakudya chimene inu simuchidziwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Iye anawawuza kuti, “Ine ndili ndi chakudya choti ndidye chimene inu simukuchidziwa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iye anati kwa iwo, Ine ndiri naco cakudya cimene inu simucidziwa.