John 4:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo ophunzirawo adayamba kufunsana kuti, “Kodi kapena wina wadzaŵapatsa kale chakudya?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake ophunzira ananena wina ndi mnzake, Kodi pali wina anamtengera Iye kanthu kakudya?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ophunzira ake anafunsana wina ndi mnzake kuti, “Kodi alipo wina amene anamubweretsera Iye chakudya?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace ophunzira ananena wina ndi mnzace, Kodi pali wina anamtengera iye kanthu kakudya?