John 4:37 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja amanenadi zoona aja amati, ‘Wobzala ndi wina, wokolola ndi winanso.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti m'menemo chonenacho chili choona, Wofesa ndi wina, womweta ndi winanso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake mawu akuti, ‘Wina amafesa ndipo wina amakolola’ ndi woona.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti m'menemo conenaco ciri coona, Wofesa ndi wina, womweta ndi winanso.