John 4:43 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atapita masiku aŵiriwo, Yesu adachoka napita ku Galileya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma atapita masiku awiriwo anachoka komweko kunka ku Galileya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Patatha masiku awiri Iye anachoka napita ku Galileya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma atapita masiku awiriwo anacoka komweko kunka ku Galileya.