John 4:49 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndunayo idati, “Ndapota nanu Ambuye, tiyeni mwana wanga asanafe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mkuluyo ananena kwa Iye, Ambuye, tsikani asanafe mwana wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nduna ya mfumuyo inati, “Ambuye tiyeni mwana wanga asanafe.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mkuluyo ananena kwa iye, Ambuye, tsikani asanafe mwana wanga.