John 4:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵiyo nkuti ophunzira ake aja atakagula chakudya mu mzinda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ophunzira ake adachoka kunka kumudzi kuti akagule chakudya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
(Ophunzira ake nʼkuti atapita mʼmudzi kukagula chakudya).
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ophunzira ace adacoka kunka kumudzi kuti akagule cakudya.