John 5:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atate saweruza munthu aliyense, koma adaika Mwana wake kuti akhale woweruza pa zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Atate saweruza munthu aliyense, koma anapereka kuweruza konse kwa Mwana;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komanso, Atate saweruza aliyense koma wapereka kwa Mwana ulamuliro woweruzawo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Atate saweruza munthu ali yense, koma anapereka kuweruza konse kwa Mwana;