John 5:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adapatsa Mwanayo mphamvu ya kuweruza anthu, chifukwa ndi Mwana wa Munthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo anampatsa Iye mphamvu ya kuchita mlandu, pakuti ali Mwana wa Munthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo wamupatsa Iye ulamuliro woweruza chifukwa ndi Mwana wa Munthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo anampatsa iye mphamvu ya kucita mlandu, pakuti ali Mwana wa munthu.