John 5:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'makondemo munkagona anthu ambiri odwala, akhungu, opunduka miyendo ndi opuwala ziwalo. [Iwoŵa ankadikira kuti madzi agwedezeke.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'menemo munagona khamu lalikulu la anthu odwala, akhungu, opunduka miyendo, opuwala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼmenemo munkagonamo gulu lalikulu la anthu odwala, osaona, olumala ndi ofa ziwalo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'menemo munagona khamu lalikuru la anthu odwala akhungu, opunduka miyendo, opuwala. [