John 5:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ngati ndidzichitira ndekha umboni, umboni wangawo ngwosakwanira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati ndichita umboni wa Ine ndekha, umboni wanga suli woona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngati ndidzichitira umboni ndekha, umboni wanga si woona.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati ndicita umboni wa Ine ndekha, umboni wanga suli woona.