John 5:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yohane anali ngati nyale yoyaka ndi yoŵala, ndipo inu mudafuna kukondwerera kuŵala kwakeko pa kanthaŵi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iyeyo anali nyali yoyaka ndi yowala; ndipo inu munafuna kukondwera m'kuunika kwake kanthawi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yohane anali ngati nyale imene imayaka ndi kuwala, ndipo inu kwa kanthawi munasankha kusangalala ndi kuwala kwakeko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iyeyo anali nyali yoyaka ndi yowala; ndipo inu munafuna kukondwera m'kuunika kwace kanthawi.