John 5:40 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe inu simufuna kudza kwa Ine kuti mukhale ndi moyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo simufuna kudza kwa Ine, kuti mukhale nao moyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma inu mukukana kubwera kwa Ine kuti mukhale ndi moyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo 3 simufuna kudza kwa Ine, kuti mukhale nao moyo.