John 5:42 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ndikukudziŵani, mulibe chikondi cha Mulungu mumtima mwanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ndikudziwani inu, kuti mulibe chikondi cha Mulungu mwa inu nokha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
koma Ine ndikukudziwani. Ndikudziwa kuti mʼmitima mwanu mulibe chikondi cha Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ndikudziwani inu, kuti mulibe cikondiea Mulungu mwa inu nokha.