John 5:44 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukamapatsana ulemu nokhanokha mumasangalala, koma simufuna konse kulandira ulemu wochokera kwa amene Iye yekha ndiye Mulungu. Nanga mungakhulupirire bwanji?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mungathe inu bwanji kukhulupirira, popeza mulandira ulemu wina kwa mnzake ndipo ulemu wakuchokera kwa Mulungu yekha simuufuna?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi inu mudzakhulupirira bwanji ngati mumapatsana ulemu wina ndi mnzake, ndipo simufuna kulandira ulemu kuchokera kwa Mulungu yekhayo?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mungathe inu bwanji kukhulupira, 5 popeza mulandira ulemu wina kwa mnzace ndipo ulemu wakucokera kwa Mulungu yekha simuufuna?