John 5:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pompo munthuyo adachiradi, nanyamula mphasa yake nkuyamba kuyenda. Tsikulo linali la Sabata.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pomwepo munthuyu anachira, nayalula mphasa yake, nayenda. Koma tsiku lomwelo linali la Sabata.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthawi yomweyo munthuyo anachiritsidwa. Iye ananyamula mphasa yake nayamba kuyenda. Tsiku limene izi zinachitika linali la Sabata.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pomwepo munthuyu anacira, nayalula mphasa yace, nayenda. Koma tsiku lomwelo linali la Sabata.