John 6:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adatoladi zotsala zonse za buledi msanu uja, nadzaza madengu khumi ndi aŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pomwepo anasonkhanitsa, nadzaza madengu khumi ndi awiri ndi makombo a mikate isanuyo yabarele, amene anatsalira anadyawo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho iwo anasonkhanitsa makombo nadzaza madengu khumi ndi awiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pomwepo anasonkhanitsa, nadzaza mitanga khumi ndi iwiri ndi makombo a mikate isanuyo yabarele, amene anatsalira anadyawo.