John 6:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'mene kunkayamba kuda, ophunzira ake a Yesu adatsikira ku nyanja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pofika madzulo, ophunzira ake anatsikira kunyanja;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pofika madzulo, ophunzira ake anatsikira ku nyanja,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pofika madzulo, akuphunzira ace anatsikira kunyanja;