John 6:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumeneko adaloŵa m'chombo, nayamba kuwoloka nyanja kupita ku Kapernao. Mdima udagwa, Yesu osafikabe kwa iwo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo pamene adalowa m'ngalawa, analikuoloka nyanja kunka ku Kapernao. Ndipo kutada pamenepo, koma Yesu asanadze kwa iwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kumene iwo analowa mʼbwato ndi kuyamba kuwoloka nyanja kupita ku Kaperenawo. Tsopano kunali kutada ndipo Yesu anali asanabwerere kwa iwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo pamene adalowa m'ngalawa, analikuoloka nyanja kunka ku Kapernao. Ndipo kutada pamenepo, koma Yesu asanadze kwa iwo.