John 6:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komanso nyanja idaavwanduka, chifukwa mphepo inkaomba kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo nyanja inalikuuka chifukwa cha mphepo yaikulu yakuombako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mphepo yamphamvu inawomba ndipo nyanja inalusa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo nyanja inalikuuka cifukwa ca mphepo yaikulu yakuombako.