John 6:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atapalasa chombo ulendo wokwanira mitunda itatu kapena inai, adaona Yesu akuyenda pa madzi nkumayandikira ku chombo chao, motero iwowo adachita mantha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene adapalasa monga mastadiya makumi awiri ndi asanu kapena makumi atatu, anaona Yesu alikuyenda panyanja, ndi kuyandikira ngalawa; ndipo anachita mantha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo atayenda makilomita asanu kapena asanu ndi limodzi, anaona Yesu akuyandikira bwatolo, akuyenda pa madzi; ndipo anachita mantha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo parnene adapalasa monga mastadiya makumi awiri ndi asanu kapena makumi atatu, anaona Yesu alikuyenda panyanja, ndi kuyandikira ngalawa; ndipo anacita mantha.