John 6:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe zombo zina zochokera ku Tiberiasi zidafika pafupi ndi malo amene anthu aja adaadyera chakudya Ambuye atayamika Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma zinachokera ngalawa zina ku Tiberiasi, pafupi pa malo pomwe adadyapo mkate m'mene Ambuye Yesu adayamika;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka mabwato ena ochokera ku Tiberiya anafika pafupi ndi pamalo pamene anthu anadya buledi Ambuye atayamika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma zinacokera ngalawa zina ku Tiberiya, pafupi pa malo pomwe adadyapo mkate m'mene Yesu adayamika;