John 6:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene anthu aja adampeza Yesu kutsidya kwa nyanja, adamufunsa kuti, “Aphunzitsi, mudafika liti kuno?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene anampeza Iye tsidya lina la nyanja, anati kwa Iye, Rabi, munadza kuno liti?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atamupeza mbali ina ya nyanjayo, iwo anamufunsa Iye kuti, “Rabi, mwafika nthawi yanji kuno?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene anampeza iye tsidya lina la nyanja, anati kwa iye, Rabi, munadza kuno liti?