John 6:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo anthu aja adayamba kufunsana kuti, “Titanitu tsono kuti titsate bwino zimene Mulungu afuna?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anati kwa Iye, Tichite chiyani, kuti tichite ntchito za Mulungu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anamufunsa Iye kuti, “Kodi tichite chiyani kuti tigwire ntchito za Mulungu?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anati kwa iye, Ticite ciani, kuti ticite nchito za Mulungu?