John 6:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Makolo athu ankadya mana m'chipululu muja, monga Malembo akunenera kuti, ‘Ankaŵapatsa chakudya chochokera Kumwamba kuti adye.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atate athu anadya mana m'chipululu; monga kwalembedwa, Mkate wochokera m'mwamba anawapatsa iwo kudya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Makolo athu akale anadya mana mʼchipululu; monga zalembedwa: ‘anawapatsa buledi wochokera kumwamba kuti adye.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atate athu anadya mana m'cipululu; monga kwalembedwa, Mkate wocokera m'mwamba anawapatsa iwo kudya,